Press "Enter" to skip to content

Tiyende Pamodzi – Kenneth Kaunda

Tiyende Pamodzi ndim’tima umo,
Tiyende Pamodzi ndim’tima umo,
Tiyende Pamodzi ndim’tima umo,
Tiyende Pamodzi ndim’tima umo.

A yuthi tiye Limbo moyo,
A yuthi tiye Limbo moyo,
Tiyende pamodzi ndim’tima umo.
A yuthi tiye Limbo moyo,
A yuthi tiye Limbo moyo,
Tiyende pamodzi ndim’tima umo.

Tioloke Limpopo ndim’tima umo,
Tioloke Limpopo ndim’tima umo,
Tioloke Limpopo ndim’tima umo,
Tioloke Limpopo ndim’tima umo.

Comex Tiyende, Limbo Moyo,
Comex Tiyende, Limbo Moyo,
Tioloke Limpopo ndim’tima umo.
Comex Tiyende, Limbo moyo,
Comex Tiyende, Limbo moyo,

Tiyende pamodzi ndim’tima umo.

 

Be First to Comment

    Leave a Reply

    This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.